2 Kings 18:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa milungu ya anthu a mitundu ina, kodi alipo ndi mmodzi yemwe amene adapulumutsapo dziko lake kwa mfumu ya ku Asiriya?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mulungu uliwonse wa amitundu walanditsa dziko lake m'dzanja la mfumu ya Asiriya ndi kale lonse?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mulungu wa anthu a mtundu wina uliwonse wapulumutsapo dziko lake mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mlungu uli wonse wa amitundu walanditsa dziko lace m'dzanja la mfumu ya Asuri ndi kale lonse?