2 Kings 18:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi milungu ya Hamati ndi Aripadi ili kuti? Nanga milungu ya Sefaravaimu, Hena ndi Iva ili kuti? Kodi milunguyo idaupulumutsa mzinda wa Samariya kwa mbuye wanga?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ili kuti milungu ya Hamati, ndi ya Aripadi? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu, kapena Hena, ndi Iva? Kodi yalanditsa Samariya m'dzanja langa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ili kuti milungu ya Hamati ndi Aripadi? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu, Hena ndi Ivani? Kodi inapulumutsa Samariya mʼdzanja langa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iri kuti milungu ya Hamati, ndi ya Aripadi? iri kuti milungu ya Sefaravaimu, kapena Hena, ndi Iva? Kodi yalanditsa Samariya m'dzanja langa?