2 Kings 18:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu adangokhala chete, osayankhapo kanthu chifukwa mfumu Hezekiya adaaŵalamula kuti, “Musamuyankhe ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthuwo anakhala chete osamyankha mau; pakuti lamulo la mfumu ndilo kuti, Musamuyankha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu anakhala chete ndipo sanayankhepo kanthu, chifukwa mfumu inawalamula kuti, “Musayankhe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthuwo anakhala cete osamyankha mau; pakuti lamulo la mfumu ndilo kuti, Musamuyankha.