2 Kings 18:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hezekiyayo adakhulupirira Chauta, Mulungu wa Aisraele, kotero kuti panalibe wofanafana naye pakati pa mafumu onse a ku Yuda iyeyo atafa, ngakhale pakati pa amene analipo kale iye asanaloŵe ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakhulupirira Yehova Mulungu wa Israele; atafa iye panalibe wakunga iye mwa mafumu onse a Yuda, ngakhale mwa iwo okhalapo asanabadwe iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya anadalira Yehova Mulungu wa Israeli. Kotero panalibe wina wofanana naye pakati pa mafumu onse a Yuda, asanakhale mfumu kapena atakhala kale mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakhulupirira Yehova Mulungu wa Israyeli; atafa iye panalibe wakunga iye mwa mafumu onse a Yuda, ngakhale mwa iwo okhalapo asanabadwe iye.