2 Kings 18:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta anali naye. Kulikonse kumene ankapita, zinthu zinkamuyendera bwino. Hezekiyayo adapandukira mfumu ya ku Asiriya, mwakuti sankaitumikiranso ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anali naye, nachita iye mwanzeru kulikonse anamukako, napandukira mfumu ya Asiriya osamtumikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anali naye ndipo kulikonse kumene anapita zinthu zinkamuyendera bwino. Iye anagalukira mfumu ya ku Asiriya ndipo sanayitumikirenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anali naye, nacita iye mwanzeru kuli konse anamukako, napandukira mfumu ya Asuri osamtumikira.