2 Kings 18:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakantha Afilisti mpaka ku Gaza ndi ku dera lake lonse. Adaononga mudzi uliwonse ndi mzinda uliwonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakantha Afilisti mpaka Gaza ndi malire ake, kuyambira nsanja ya olonda mpaka mudzi walinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakantha Afilisti kuyambira ku nsanja ya alonda mpaka ku mzinda wotetezedwa. Anakafika mpaka ku Gaza ndi ku malire ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakantha Afilisti mpaka Gaza ndi malire ace, kuyambira nsanja ya olonda mpaka mudzi walinga.