2 Kings 19:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga mafumu a m'mizinda ya Hamati, Aripadi, Separavaimu ndi Iva ali kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ili kuti mfumu ya Hamati, ndi mfumu ya Aripadi, ndi mfumu ya mudzi wa Sefaravaimu, wa Hena, ndi Iva?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mafumu a Hamati, Aripadi ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena ndi Iva, ali kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iri kuti mfumu ya Hamati, ndi mfumu ya Aripadi, ndi mfumu ya mudzi wa Sefaravaimu, wa Hena, ndi Iva?