2 Kings 19:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, zoonadi mafumu a ku Asiriya adaononga anthu a mitundu ina yonse, nasandutsa maiko ao chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zoona, Yehova, mafumu a Asiriya anapasula amitundu ndi maiko ao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu Yehova, nʼzoonadi kuti mafumu a Asiriya anawononga mitundu iyi ndi mayiko awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zoona, Yehova, mafumu a Asuri anapasula amitundu ndi maiko ao,