2 Kings 19:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesaya mwana wa Amozi adatumiza kwa mfumu Hezekiya mau omuuza kuti Chauta, Mulungu wa Israele, wamva pemphero lake lija lonena za Senakeribu mfumu ya ku Asiriya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yesaya mwana wa Amozi anatumiza kwa Hezekiya, ndi kuti, Atero Yehova Mulungu wa Israele, Chondipempha iwe pa Senakeribu mfumu ya Asiriya ndachimva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya wakuti, “Yehova Mulungu wa Israeli akuti, ‘Ndamva pemphero lako lonena za Senakeribu mfumu ya ku Asiriya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yesaya mwana wa Amozi anatumiza kwa Hezekiya, ndi, kuti, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Condipempha iwe pa Sanakeribu mfumu ya Asuri ndacimva.