2 Kings 19:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poitsutsa mfumuyo Chauta adati, “Mzinda wa Ziyoni ukukunyoza ndi kukuseka, iwe Senakeribu, mzinda wa Yerusalemu ukupukusa mutu kumbuyo kwako monyodola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a Yehova akumnenera iye ndi awa, Namwali mwana wamkazi wa Ziyoni akunyoza, akuseka mwana wamkazi wa Yerusalemu, akupukusira mutu pambuyo pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu amene Yehova wayankhula wotsutsana naye ndi awa: “Namwali wa Ziyoni akukunyoza ndi kukuseka iwe. Mwana wamkazi wa Yerusalemu akupukusa mutu wake kumbuyo kwako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a Yehova akumnenera iye ndi awa, Namwali mwana wamkazi wa Ziyoni akunyoza, akuseka mwana wamkazi wa Yerusalemu, akupukusira mutu pambuyo pako.