2 Kings 19:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakumba zitsime ku maiko achilendo ndi kumwamo madzi. Ndi mapazi anga ndidapondereza ndi kuumitsa mitsinje ya ku Ejipito.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndakapa, ndamwa madzi achilendo, ndi ku mapazi anga ndidzaphwetsa mitsinje yonse ya Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakumba zitsime ku mayiko achilendo ndipo ndinamwa madzi a kumeneko. Ndi mapazi anga ndawumitsa mitsinje yonse ya ku Igupto.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndakapa, ndamwa madzi acilendo, ndi ku mapazi anga ndidzaphwetsa mitsinje yonse ya Aigupto,