2 Kings 19:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma Ine ndimadziŵa zonse za iwe, pamene ukhala pansi, pamene uyenda kwina ndi kubwerako, ndiponso pamene undikwiyira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndidziwa kukhala pansi kwako, ndi kutuluka kwako, ndi kulowa kwako, ndi kundizazira kwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Koma Ine ndimadziwa kukhala kwako, kutuluka kwako ndi kulowa kwako, ndi mkwiyo wako pa Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidziwa kukhala pansi kwako, ndi kuturuka kwako, ndi kulowa kwako, ndi kundizazira kwako.