2 Kings 19:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a m'banja la Yuda amene adzatsalire adzapezanso bwino, ngati zomera zimene zazamitsa mizu pansi ndi kubala zipatso poyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo opulumuka a nyumba ya Yuda otsalawo adzaphukanso mizu, ndi kupatsa zipatso pamwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a nyumba ya Yuda amene adzatsale adzazika mizu ndi kubereka zipatso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo opulumuka a nyumba ya Yuda otsalawo adzaphukanso mizu, ndi kupatsa zipatso pamwamba.