2 Kings 19:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidzautchinjiriza ndi kuuteteza mzinda umenewu chifukwa cha ulemerero wanga, ndiponso chifukwa cha chipangano changa chimene ndidachita ndi Davide mtumiki wanga.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidzatchinjiriza mudzi uno kuupulumutsa, chifukwa cha Ine mwini, ndi chifukwa cha Davide mtumiki wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzateteza mzinda umenewu kuwupulumutsa, chifukwa cha Ine mwini ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidzacinjiriza mudzi uno kuupulumutsa, cifukwa ca Ine mwini, ndi cifukwa ca Davide mtumiki wanga.