2 Kings 19:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Senakeribu, mfumu ya ku Asiriya, adachoka ndi kubwerera kwao, nakakhala ku Ninive.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nachoka Senakeribu mfumu ya Asiriya, namuka, nabwerera, nakhala ku Ninive.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Senakeribu mfumu ya ku Asiriya anapasula misasa ndi kuchoka. Anabwerera ku Ninive nakakhala kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nacoka Sanakeribu mfumu ya Asuri, namuka, nabwerera, nakhala ku Nineve.