2 Kings 2:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idafika nthaŵi imene Chauta adafuna kutenga Eliya m'kamvulumvulu kunka kumwamba. Tsiku limenelo Eliya ndi Elisa anali pa ulendo kuchokera ku Giligala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pamene Yehova adati akweze Eliya kumwamba ndi kamvulumvulu, Eliya anachokera ku Giligala pamodzi ndi Elisa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ali pafupi kutenga Eliya kupita kumwamba mu kamvuluvulu, Eliya ndi Elisa anali pa ulendo wopita ku Giligala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pamene Yehova adati akweze Eliya kumwamba ndi kabvumvulu, Eliya anacokera ku Giligala pamodzi ndi Elisa.