2 Kings 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adabwerera kwa Elisayo pamene iyeyo ankadikira ku Yeriko, ndipo iye adaŵauza kuti, “Kodi suja ndidaanena kuti musapite?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nabwerera kwa iye ali chikhalire ku Yeriko, ndipo anati kwa iwo, Kodi sindinanena nanu, Musamuka?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atabwerera kwa Elisa (chifukwa anali akanali ku Yeriko), iye anawawuza kuti, “Kodi sindinakuwuzeni kuti musapite?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nabwerera kwa iye ali cikhalire ku Yeriko, ndipo anati kwa iwo, Kodi sindinanena nanu, Musamuka?