2 Kings 2:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero madziwo ngabwinobe kwambiri mpaka lero lino, potsata mau amene Elisa adaalankhula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chotero madzi anachiritsidwa mpaka lero lino, monga mwa mau a Elisa ananenawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero madziwo ndi abwino mpaka lero, molingana ndi mawu amene Elisa anayankhula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cotero madzi anaciritsidwa mpaka lero lino, monga mwa mau a Elisa ananenawo.