2 Kings 2:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atachoka kumeneko, Elisa adapitirira kunka ku phiri la Karimele, ndipo pochoka kumeneko adabwerera ku Samariya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachokako kunka kuphiri la Karimele; nabwera kumeneko nafika ku Samariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anapita ku phiri la Karimeli. Pochoka kumeneko anabwerera ku Samariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacokako kumka ku phiri la Karimeh; nabwera kumeneko nafika ku Samariya.