2 Kings 2:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu makumi asanu a m'gulu la aneneri aja adapita nawo ndipo adakaimirira chapatali potero, pamene Eliya ndi Elisa adaakaima pa gombe la mtsinje wa Yordani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu makumi asanu a ana a aneneri anapita, naima patali pandunji pao, iwo awiri naima ku Yordani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu makumi asanu mwa ana a aneneri anawatsatira nayima chapatali moyangʼanana nawo ndipo Eliya ndi Elisa anayima mʼmphepete mwa Yorodani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu makumi asanu a ana a aneneri anapita, naima patali pandunji pao, iwo awiri naima ku Yordano.