2 Kings 20:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yesaya adauza Hezekiya kuti, “Chauta akunena kuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yesaya anati kwa Hezekiya, Tamverani mau a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yesaya anawuza Hezekiya kuti, “Imvani zimene Yehova akunena:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yesaya anati kwa Hezekiya, Tamverani mau a Yehova.