2 Kings 20:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Hezekiya adamwalira naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo ake. Tsono Manase mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Hezekiya ndi makolo ake; nakhala mfumu m'malo mwake Manase mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya anamwalira nagona pamodzi ndi makolo ake. Ndipo Manase mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Hezekiya ndi makolo ace; nakhala mfumu m'malo mwace Manase mwana wace.