2 Kings 20:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesaya asanatuluke m'bwalo lapakati, Chauta adamuuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, asanatulukire Yesaya m'kati mwa mudzi, anamdzera mau a Yehova, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesaya asanatuluke mʼbwalo lapakati, Yehova anayankhula kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, asanaturukire Yesaya m'kati mwa mudzi, anamdzera mau a Yehova, ndi kuti,