2 Kings 21:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anyamata ake adamchita chiwembu, namupha m'nyumba mwake momwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata ake a Amoni anamchitira chiwembu, napha mfumuyo m'nyumba yakeyake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nduna za Amoni zinamuchita chiwembu ndipo zinamupha mʼnyumba yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata ace a Amoni anamcitira ciwembu, napha mfumuyo m'nyumba yace yace.