2 Kings 22:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo idalamula wansembe Hilikiya, Ahikamu mwana wa Safani, Akibori mwana wa Mikaya, Safani mlembi uja ndi Asaya mtumiki wa mfumu, kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inalamulira Hilikiya wansembe, ndi Ahikamu mwana wa Safani, ndi Akibori mwana wa Mikaya, ndi Safani mlembi, ndi Asaya mnyamata wa mfumu, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyo inalamula wansembe Hilikiya, Ahikamu mwana wa Safani, Akibo mwana wa Mikaya, Safani mlembi uja ndi Asaiya mtumiki wa mfumu, kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inalamulira Hilikiya wansembe, ndi Ahikamu mwana wa Safani, ndi Alabori mwana wa Mikaya, ndi Safani mlembi, ndi Asaya mnyamata wa mfumu, ndi kuti,