2 Kings 22:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
iyeyo adaŵauza kuti, “Chauta, Mulungu wa Israele, akunena kuti, ‘Muuzeni munthu wakutumani kwa Ineyo kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hulida ananena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israele, Muuze munthuyo anakutumizani kwa ine,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anawawuza kuti, “Yehova Mulungu wa Israeli akuti: Kamuwuzeni munthu amene wakutumani kwa ine kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hulida ananena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Muuze munthuyo anakutumizani kwa ine,