2 Kings 22:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 18 cha ufumu wake, Yosiya adatuma Safani mwana wa Azaliya, mwana wa Mesulamu, mlembi wa ku Nyumba ya Chauta, nati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yosiya, mfumuyi inatuma Safani mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu, mlembi, kunyumba ya Yehova, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 18 cha ufumu wake, Mfumu Yosiya anatuma mlembi wa nyumba ya mfumu, Safani, mwana wa Azariya, mwana wa Mesulamu, ku Nyumba ya Yehova. Iye anati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yosiya, mfumuyi inatuma Safani mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu, mlembi, ku nyumba ya Yehova, ndi kuti,