2 Kings 22:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndalama zimenezo azipereke kwa akapitao okonzetsa Nyumba ya Chauta aja. Iwowo azipereke kwa antchito aja okonza Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwo azipereke kwa ogwira ntchito ya m'nyumba ya Yehova, akonze mogamuka nyumbayi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndalamazo azipereke kwa anthu amene asankhidwa kuti ayangʼanire ntchito ya Nyumba ya Yehova. Ndipo anthu amenewa azilipira antchito amene akukonzanso Nyumba ya Yehova,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwo azipereke kwa ogwira nchito ya m'nyumba ya Yehova, akonze mogamuka nyumbayi,