2 Kings 22:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu amene apatsidwe ndalama zolipirira antchito okonza Nyumbawo asaŵafunse kuti afotokoze za kamwazidwe ka ndalamazo, popeza kuti ndi anthu okhulupirika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sanawawerengere ndalamazo zoperekedwa m'dzanja lao, pakuti anachita mokhulupirika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu amene apatsidwa ndalama zolipira antchito okonza Nyumbayo asawafunse za kagwiritsidwe ntchito ka ndalamazo, popeza ndi anthu wokhulupirika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sanawawerengera ndalamazo zoperekedwa m'dzanja lao, pakuti anacita mokhulupirika.