2 Kings 22:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Safani mlembi uja adapita kwa mfumu, nakafotokozera mfumuyo kuti, “Atumiki anu atenga ndalama zija zinali m'Nyumbazi, ndipo azipereka kwa anthu amene akuyang'anira ntchito yokonza Nyumba ya Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Safani mlembiyo anadza kwa mfumu, nambwezera mfumu mau, nati, Anyamata anu anakhuthula ndalama zopereka m'nyumba, nazipereka m'dzanja la antchito akuyang'anira nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Safani mlembi uja, anapita nakafotokozera mfumu kuti, “Atumiki anu apereka ndalama zija zinali mʼNyumba ya Yehova kwa anthu amene akugwira ntchito ndi kuyangʼanira ntchito yokonza Nyumba ya Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Safani mlembiyo anadza kwa mfumu, nambwezera mfumu mau, nati, Anyamata anu anakhuthula ndalama zopereka m'nyumba, nazipereka m'dzanja la anchito akuyang'anira nyumba ya Yehova.