2 Kings 23:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu Yosiya adalamula anthu onse kuti, “Muchite chikondwerero cha Paska, kulemekeza Chauta, Mulungu wanu, potsata zimene zidalembedwa m'buku lachipangano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inalamulira anthu onse, kuti, Mchitireni Yehova Mulungu wanu Paska, monga mulembedwa m'buku ili la chipangano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inalamula anthu onse kuti, “Chitani Chikondwerero cha Paska kulemekeza Yehova Mulungu wanu, motsatira zomwe zalembedwa mʼBuku la Chipangano.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inalamulira anthu onse, kuti, Mcitireni Yehova Mulungu wanu Paskha, monga mulembedwa m'buku ili la cipangano,