2 Kings 23:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adagwetsa tinyumba ta amuna ochitana zadama ku Nyumba ya Mulungu, ku malo amene akazi ankalukira mikanjo yovala anthu opembedza Asera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagamula nyumba za anyamata adama okhala kunyumba ya Yehova, kumene akazi anaomba nsalu zolenjeka za chifanizocho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anagwetsanso tinyumba ta ochita zachiwerewere, timene tinali mʼNyumba ya Yehova, kumene akazi ankalukirako mikanjo yovala popembedza Asera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagamula nyumba za anyamata adama okhala ku nyumba ya Yehova, kumene akazi anaomba nsaru zolenjeka za cifanizoco.