2 Kings 24:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatenga chuma chonse cha ku Nyumba ya Chauta, pamodzi ndi chuma chonse cha ku nyumba ya mfumu. Adaononga ziŵiya zonse zagolide za ku Nyumba ya Chauta zimene Solomoni mfumu ya ku Israele adapanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natulutsa kuchotsa komweko chuma chonse cha nyumba ya Yehova, ndi chuma cha nyumba ya mfumu, naduladula zipangizo zonse zagolide adazipanga Solomoni mfumu ya Israele m'Kachisi wa Yehova, monga Yehova adanena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga ananenera Yehova, Nebukadinezara anachotsa chuma chonse cha mʼNyumba ya Yehova ndiponso cha mʼnyumba ya mfumu ndipo anatenga ziwiya zonse zagolide za ku Nyumba ya Yehova zimene Solomoni mfumu ya Israeli anapanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naturutsa kucotsa komweko cuma conse ca nyumba ya Yehova, ndi cuma ca nyumba ya mfumu, naduladula zipangizo zonse zagolidi adazipanga Solomo mfumu ya Israyeli m'Kacisi wa Yehova, monga Yehova adanena.