2 Kings 24:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso chifukwa cha magazi a anthu osachimwa amene iye adakhetsa. Manaseyu adadzaza Yerusalemu ndi magazi a anthu osachimwa, ndipo Chauta sadamkhululukire ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiponso chifukwa cha mwazi wosachimwa adaukhetsa; popeza anadzaza Yerusalemu ndi mwazi wosachimwa; ndipo Yehova sanafune kukhululukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuphatikizapo kukhetsa magazi a anthu osalakwa. Chifukwa iye anadzaza Yerusalemu ndi magazi a anthu osalakwa ndipo Yehova sanafune kumukhululukira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiponso cifukwa ca mwazi wosacimwa adaukhetsa; popeza anadzaza Yerusalemu ndi mwazi wosacimwa; ndipo Yehova sanafuna kukhululukira.