2 Kings 25:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mkulu wa asilikaliyo adasiyako anthu ena osauka kwambiri am'dzikomo, kuti azisamala minda yamphesa ndi minda ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mkulu wa olindirira anasiya osaukadi a m'dziko akhale osunga minda yampesa, ndi alimi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mkulu wa asilikaliyo anasiya anthu ena osauka kwambiri mʼdzikomo kuti azisamalira minda ya mpesa ndi minda ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mkuru wa olindirira anasiya osaukadi a m'dziko akhale osunga minda yampesa, ndi alimi,