2 Kings 25:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkulu wa asilikali uja adatenganso ziwaya zosonkhapo moto ndiponso mbale zowazira madzi, ndi zina zonse zagolide ndi zasiliva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi zopalira moto, ndi mbale zowazira za golide yekhayekha, ndi zasiliva yekhayekha, mkulu wa asilikali anazichotsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkulu wa asilikali uja anatenganso zofukizira lubani ndi mbale zowazira magazi. Zonsezi zinali zopangidwa ndi golide wabwino kwambiri kapena siliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi zoparira moto, ndi mbale zowazira za golidi yekha yekha, ndi zasiliva yekha yekha, mkuru wa asilikari anazicotsa.