2 Kings 25:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za nsanamira ziŵiri zija, chimbiya, ndi maphaka zimene Solomoni adaapangira Nyumba ya Chauta, kulemera kwake kwa mkuŵa wa zonsezo kunali kosaŵerengeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsanamira ziwiri, thawale limodzi, ndi maphakawo adazipangira nyumba ya Yehova Solomoni, mkuwa wa zipangizo izi zonse sanakhoze kuyesa kulemera kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkuwa wochokera ku zipilala ziwiri zija, mbiya ija ndi maphaka aja, zimene Solomoni anapanga mʼNyumba ya Yehova, kuchuluka kwake kunali kosawerengeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsanamira ziwiri, thawale limodzi, ndi maphakawo adazipangira nyumba ya Yehova Solomo, mkuwa wa zipangizo izi zonse sanakhoza kuyesa kulemera kwace.