2 Kings 25:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni adaika Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani, kuti akhale kazembe woyang'anira anthu otsala aja amene Nebukadinezarayo adaŵasiya ku dziko la Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunena za anthu otsalira m'dziko la Yuda, amene adawasiya Nebukadinezara mfumu ya Babiloni, iyeyu anamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani akhale wowalamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nebukadinezara mfumu ya Babuloni anasankha Gedaliya mwana wa Ahikamu, mwana wa Safani, kukhala woyangʼanira anthu amene anatsala ku Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunena za anthu otsalira m'dziko la Yuda, amene adawasiya Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iyeyu anamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani akhale wowalamulira.