2 Kings 25:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo pamodzi ndi anthu ao, Gedaliya adaŵalonjeza molumbira kuti, “Musaope chifukwa cha atsogoleri a Ababiloniwo. Khalani m'dzikomu, muzimvera mfumu ya ku Babiloni, ndipo zinthu zidzakuyenderani bwino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nawalumbirira Gedaliya iwo ndi anthu ao, nanena nao, Musamaopa anyamata a Ababiloni; khalani m'dziko; tumikirani mfumu ya Babiloni, ndipo kudzakukomerani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gedaliya analumbira powatsimikizira iwo ndi anthu awo. Iye anati, “Musachite mantha ndi atsogoleri Ababuloniwa. Khalani mʼdziko muno ndipo tumikirani mfumu ya Babuloni. Mukatero zinthu zidzakuyenderani bwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawalumbirira Gedaliya iwo ndi anthu ao, nanena nao, Musamaopa anyamata a Akasidi; khalani m'dziko; tumikirani mfumu ya Babulo, ndipo kudzakukomerani.