2 Kings 25:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Aisraele onse, olemera ndi osauka omwe, pamodzi ndi atsogoleri ankhondo, adanyamuka kupita ku Ejipito, poti ankaopa Ababiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ananyamuka anthu onse ang'ono ndi akulu, ndi akazembe a makamu, nadza ku Ejipito; pakuti anaopa Ababiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha zimenezi, anthu onse kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, pamodzi ndi atsogoleri a ankhondo anathawira ku Igupto chifukwa choopa Ababuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananyamuka anthu onse ang'ono ndi akuru, ndi akazembe a makamu, nadza ku Aigupto; pakuti anaopa Akasidi.