2 Kings 25:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamchitira zabwino, namkweza kupambana mafumu ena onse amene anali naye limodzi ku Babiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakamba naye zokoma, namkweza mpando wake waulemu upose mipando ya mafumu anali pamodzi naye m'Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamukomera mtima namukweza kupambana mafumu ena onse amene anali naye ku Babuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakamba naye zokoma, namkweza mpando wace waulemu upose mipando ya mafumu anali pamodzi naye m'Babulo.