2 Kings 25:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pa tsiku lachisanu ndi chinai pa mwezi wachinai chaka chimenecho, pamene njala inali itakula kwambiri mumzindamo, kotero kuti anthu analibiretu chakudya m'dzikomo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachisanu ndi chinai la mwezi wachinai njala idakula m'mudzimo, panalibe chakudya kwa anthu a m'dzikomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachisanu ndi chinayi pa mwezi wachinayi, njala inakula kwambiri mu mzindamo kotero kuti anthu analibe chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacisanu ndi cinai la mwezi wacinai njala idakula m'mudzimo, panalibe cakudya kwa anthu a m'dzikomo.