2 Kings 25:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo a ku Babiloni aja atamgwira Zedekiyayo, adapita naye kwa Nebukadinezara, ku Ribula. Komweko Nebukadinezarayo adagamula mlandu wa Zedekiya uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaigwira mfumu, nakwera nayo kwa mfumu ya Babiloni ku Ribula, naweruza mlandu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anagwidwa napita naye kwa mfumu ya ku Babuloni ku Ribula, kumene anagamula mlandu wa Zedekiyayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaigwira mfumu, nakwera nayo kwa mfumu ya Babulo ku Ribila, naweruza mlandu wace.