2 Kings 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu Yoramu adati, “Kalanga ine! Chauta waitana mafumu atatufe, kuti atipereke m'manja mwa Amowabu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya Israele inati, Kalanga ife! Pakuti Yehova waitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Mowabu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inafuwula kuti, “Nʼchiyani chomwe chikutichitikira! Kodi Yehova wasonkhanitsa mafumu atatu pamodzi kuti atipereke mʼmanja mwa Amowabu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya Israyeli inati, Kalanga ife! pakuti Yehova waitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Moabu.