2 Kings 3:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Simudzaona mphepo kapena mvula, komabe mtsinje wopanda madziwu udzadzaza ndi madzi, ndipo inuyo mudzamwa, pamodzi ndi ng'ombe zanu ndi zoŵeta zanu zina zomwe.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Yehova, Simudzaona mphepo, kapena kuona mvula, koma chigwacho chidzadzala ndi madzi; ndipo mudzamwa inu, ndi ng'ombe zanu, ndi zoweta zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova akunena kuti, ‘Simudzaona mphepo kapena mvula, komabe chigwa ichi chopanda madzi chidzadzaza ndi madzi, ndipo inu mudzamwa pamodzi ndi ngʼombe zanu ndiponso nyama zanu zonse.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Yehova, Simudzaona mphepo, kapena kuona mvula, koma cigwaco cidzadzala ndi madzi; ndipo mudzamwa inu, ndi ng'ombe zanu, ndi zoweta zanu.