2 Kings 3:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake, nthaŵi yopereka nsembe ili pafupi, adangoona madzi akutuluka kuchokera ku Edomu, mpaka malowo adadzaza madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunachitika m'mawa, pomapereka nsembe yaufa, taonani, anafika madzi odzera ku Edomu; ndipo dziko linadzala ndi madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake, nthawi yopereka nsembe ili pafupi, anangoona madzi akutuluka kuchokera ku Edomu, ndipo malo onse anadzaza ndi madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunacitika m'mawa, pomapereka nsembe yaufa, taonani, anafika madzi odzera ku Edomu; ndipo dziko linadzala ndi madzi.