2 Kings 3:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adati, “Taonani magazi! Mafumu aja amenyana okhaokha, ndipo ankhondo ao aphana. Tiyeni tikafunkhe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Uja ndi mwazi, atha kuonongana mafumu aja, anakanthana wina ndi mnzake; ndipo tsopano, tiyeni Amowabu inu, tikafunkhe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iwo anati, “Taonani magazi! Mafumu aja amenyana okhaokha ndipo aphana. Amowabu, tsopano ndi nthawi yofunkha!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, Uja ndi mwazi, atha kuonongana mafumu aja, anakanthana wina ndi mnzace; ndipo tsopano, tiyeni Amoabu inu, tikafunkhe.