2 Kings 3:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu ya Amowabu itaona kuti nkhondo yaŵaipira, idatenga anthu 700 amalupanga, kuti athaŵe modutsa ankhondo kupita kwa mfumu ya ku Edomu, koma adalephera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ataona mfumu ya Mowabu kuti nkhondo idamlaka, anapita nao anthu mazana asanu ndi awiri akusolola lupanga, kupyola kufikira kwa mfumu ya Edomu, koma sanakhoze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ya ku Mowabu itaona kuti nkhondo ikumulaka, inatenga anthu 700 a malupanga kuti athawe modutsa mfumu ya ku Edomu, koma inalephera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ataona mfumu ya Moabu kuti nkhondo idamlaka, anapita nao anthu mazana asanu ndi awiri akusolola lupanga, kupyola kufikira kwa mfumu ya Edomu, koma sanakhoza.