2 Kings 3:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Ahabu atamwalira, mfumu ya Amowabuyo idagalukira mfumu ya ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunachitika, atafa Ahabu mfumu ya Mowabu anapandukana ndi mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atamwalira Ahabu, mfumu ya ku Mowabu inawukira mfumu ya ku Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama kunacitika, atafa Ahabu mfumu ya Moabu anapandukana ndi mfumu ya Israyeli.