2 Kings 4:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina Elisa uja adafika ku Sunemu, nakaloŵa m'kachipinda kam'mwamba kaja kuti akapumule m'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo linadza tsiku lakuti anafikako, nalowa m'chipinda chosanja, nagona komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina pamene Elisa anafika ku Sunemu, iye anakalowa mʼchipinda chake chija nagona mʼmenemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo linadza tsiku lakuti anafikako, nalowa m'cipinda cosanja, nagona komweko.